Levitiko 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chaka cha 50 chidzakhala Chaka cha Ufulu kwa inu. Musadzalime minda yanu kapena kukolola mbewu zomera zokha, kapenanso kukolola mphesa zamʼmitengo yosadulira.+
11 Chaka cha 50 chidzakhala Chaka cha Ufulu kwa inu. Musadzalime minda yanu kapena kukolola mbewu zomera zokha, kapenanso kukolola mphesa zamʼmitengo yosadulira.+