Levitiko 25:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chimenecho ndi Chaka cha Ufulu ndipo chizikhala chopatulika kwa inu. Zimene mungathe kudya ndi zimene zamera zokha mʼminda yanu.+
12 Chimenecho ndi Chaka cha Ufulu ndipo chizikhala chopatulika kwa inu. Zimene mungathe kudya ndi zimene zamera zokha mʼminda yanu.+