Levitiko 25:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mukamagulitsa chinthu kwa mnzanu kapena kugula chinthu kwa mnzanu, musamachitirane chinyengo.+