Levitiko 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zadutsa kuchokera mʼChaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kuti udzalepo mbewu.+
15 Ukamagula malo kwa mnzako, uziwerenga zaka zimene zadutsa kuchokera mʼChaka cha Ufulu. Azikugulitsa malowo mogwirizana ndi zaka zimene zatsala kuti udzalepo mbewu.+