-
Levitiko 25:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Koma ngati sanaiwombole chaka chimodzicho chisanathe, nyumba imene ili mumzinda wokhala ndi mpanda izikhala ya amene anagulayo mpaka kalekale, mʼmibadwo yake yonse, ndipo isamabwezedwe mʼChaka cha Ufulu.
-