Levitiko 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Akapolowa mungathe kusiyira ana anu monga cholowa chawo mpaka kalekale. Anthu amenewa ndi amene azikhala antchito anu, koma Aisiraeli, omwe ndi abale anu musamawachitire nkhanza.+
46 Akapolowa mungathe kusiyira ana anu monga cholowa chawo mpaka kalekale. Anthu amenewa ndi amene azikhala antchito anu, koma Aisiraeli, omwe ndi abale anu musamawachitire nkhanza.+