Levitiko 25:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Komanso mchimwene wa bambo ake, mwana wa mchimwene wa bambo akewo, wachibale wake aliyense wapafupi, kapena kuti aliyense wa mʼbanja lake angathe kumuwombola. Kapenanso mwiniwakeyo akalemera, azidziwombola.+
49 Komanso mchimwene wa bambo ake, mwana wa mchimwene wa bambo akewo, wachibale wake aliyense wapafupi, kapena kuti aliyense wa mʼbanja lake angathe kumuwombola. Kapenanso mwiniwakeyo akalemera, azidziwombola.+