-
Levitiko 25:50Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
50 Kuti achite zimenezi, iye aziwerengera limodzi ndi amene anamugulayo nthawi imene yadutsa kuchokera chaka chimene anadzigulitsa kudzafika Chaka cha Ufulu.+ Ndalama zimene anamugulira zizigwirizana ndi kuchuluka kwa zakazo.+ Malipiro a ntchito imene azigwira pa nthawi yotsalayo azifanana ndi a waganyu.+
-