Levitiko 25:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma ngati sangathe kudziwombola potsatira njira zimenezi, adzachoka mʼChaka cha Ufulu,+ iye pamodzi ndi ana ake.*
54 Koma ngati sangathe kudziwombola potsatira njira zimenezi, adzachoka mʼChaka cha Ufulu,+ iye pamodzi ndi ana ake.*