Levitiko 26:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “‘Musapange milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika kuti muzichilambira. Musaike mwala wogoba+ mʼdziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:1 Mungakhale Ndi Moyo Mpaka Kalekale, lesson 19
26 “‘Musapange milungu yopanda pake,+ chifaniziro,+ kapena chipilala chopatulika kuti muzichilambira. Musaike mwala wogoba+ mʼdziko lanu kuti muziugwadira,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.