Levitiko 26:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo. Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.*
13 Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo kuti musakhale akapolo a Aiguputo. Ndinathyola goli lanu ndi kukuchititsani kuyenda mowongoka.*