Levitiko 26:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ nʼkunyansidwa ndi zigamulo zanga mpaka kukana kutsatira malamulo anga onse, nʼkufika pophwanya pangano langa,+
15 ndipo mukadzakana malangizo anga,+ nʼkunyansidwa ndi zigamulo zanga mpaka kukana kutsatira malamulo anga onse, nʼkufika pophwanya pangano langa,+