-
Levitiko 26:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Koma ngati simudzandimverabe pambuyo poona zinthu zimenezi, ndidzakulangani kuchulukitsa maulendo 7 kuposa poyamba chifukwa cha machimo anu.
-