Levitiko 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.* Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:19 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 24
19 Ndidzakuchititsani kuti musiye kunyada ndipo ndidzachititsa kumwamba kukhala ngati chitsulo+ ndi nthaka yanu ngati kopa.*