Levitiko 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mphamvu zanu zidzathera pachabe, chifukwa nthaka yanu siidzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda mwanu siidzakupatsani zipatso.
20 Mphamvu zanu zidzathera pachabe, chifukwa nthaka yanu siidzakupatsani chakudya,+ ndipo mitengo yamʼmunda mwanu siidzakupatsani zipatso.