Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzawononga njira* zanu zopezera chakudya,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi wokha, ndipo pokugawirani mkatewo, adzachita kukuyezerani+ nʼkukupatsani wochepa. Choncho mudzadya koma simudzakhuta.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:26 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 24
26 Ndikadzawononga njira* zanu zopezera chakudya,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi wokha, ndipo pokugawirani mkatewo, adzachita kukuyezerani+ nʼkukupatsani wochepa. Choncho mudzadya koma simudzakhuta.+