Levitiko 26:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mizinda yanu ndidzaiwononga+ ndi lupanga ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu, komanso sindidzalandira nsembe zanu za kafungo kosangalatsa.*
31 Mizinda yanu ndidzaiwononga+ ndi lupanga ndipo malo anu opatulika adzakhala opanda anthu, komanso sindidzalandira nsembe zanu za kafungo kosangalatsa.*