Levitiko 26:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhale bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli mʼdziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzapuma* chifukwa likuyenera kubweza masabata ake.+
34 Pa masiku onse amene dzikolo lidzakhale bwinja, lidzabweza masabata ake, inu muli mʼdziko la adani anu. Nthawi imeneyo, dziko lidzapuma* chifukwa likuyenera kubweza masabata ake.+