Levitiko 26:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati anthu amene akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha nʼkomwe kulimbana ndi adani anu.+
37 Iwo adzagwetsana okhaokha ngati anthu amene akuthawa lupanga, koma popanda munthu wowathamangitsa. Simudzatha nʼkomwe kulimbana ndi adani anu.+