Levitiko 26:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ambiri mwa inu mudzafa mʼdziko la anthu a mitundu ina,+ ndipo dziko la adani anu lidzakumezani.