Levitiko 26:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anthu amene adzatsale pakati panu adzazunzika mʼmayiko a adani awo+ chifukwa cha zolakwa zanu. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo.+
39 Anthu amene adzatsale pakati panu adzazunzika mʼmayiko a adani awo+ chifukwa cha zolakwa zanu. Iwo adzazunzika chifukwa cha zolakwa za makolo awo.+