Levitiko 26:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Kenako adzavomereza zolakwa zawo+ komanso kusakhulupirika ndi zolakwa za makolo awo. Ndipo adzavomereza kuti anachita zinthu mosakhulupirika poyenda motsutsana nane.+
40 Kenako adzavomereza zolakwa zawo+ komanso kusakhulupirika ndi zolakwa za makolo awo. Ndipo adzavomereza kuti anachita zinthu mosakhulupirika poyenda motsutsana nane.+