Levitiko 26:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Atatero, inenso ndinayenda motsutsana nawo+ ndipo ndinawapititsa kudziko la adani awo.+ Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo ingadzichepetse+ nʼkulipira chifukwa cha zolakwa zawo.
41 Atatero, inenso ndinayenda motsutsana nawo+ ndipo ndinawapititsa kudziko la adani awo.+ Izi zinachitika kuti mwina mitima yawo yosadulidwayo ingadzichepetse+ nʼkulipira chifukwa cha zolakwa zawo.