Levitiko 26:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Pa nthawi imene iwo anasiya kukhala mʼdzikomo, dzikolo linkabweza masabata ake+ ndipo linakhala bwinja iwowo kulibe. Iwo anapereka malipiro a zolakwa zawo, chifukwa anakana zigamulo zanga ndipo ananyansidwa ndi malamulo anga.+
43 Pa nthawi imene iwo anasiya kukhala mʼdzikomo, dzikolo linkabweza masabata ake+ ndipo linakhala bwinja iwowo kulibe. Iwo anapereka malipiro a zolakwa zawo, chifukwa anakana zigamulo zanga ndipo ananyansidwa ndi malamulo anga.+