45 Ndipo kuti zinthu ziwayendere bwino ndidzakumbukira pangano limene ndinachita ndi makolo awo+ amene ndinawatulutsa mʼdziko la Iguputo, anthu a mitundu ina akuona.+ Ndidzachita zimenezi kuti ndiwasonyeze kuti ndine Mulungu wawo. Ine ndine Yehova.’”