-
Levitiko 27:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Ndipo ngati munthu amene akuperekedwayo ndi wazaka zapakati pa 5 ndi 20, akakhala wamwamuna mtengo wake womwe unaikidwa ndi masekeli 20, koma akakhala wamkazi mtengo wake womwe unaikidwa ndi masekeli 10.
-