-
Levitiko 27:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Koma ngati walonjeza kupereka nyama yomwe ndi yoyenera kuperekedwa nsembe kwa Yehova, nyama iliyonse imene angapereke kwa Yehova izikhala yopatulika.
-