Levitiko 27:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mundawo ukamadzabwezedwa mʼChaka cha Ufulu, udzakhala wopatulika kwa Yehova monga munda umene waperekedwa kwa iye. Mundawo udzakhala wa ansembe.+
21 Mundawo ukamadzabwezedwa mʼChaka cha Ufulu, udzakhala wopatulika kwa Yehova monga munda umene waperekedwa kwa iye. Mundawo udzakhala wa ansembe.+