-
Levitiko 27:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Ngʼombe kapena nkhosa iliyonse ya 10, pa nyama zonse zodutsa pansi pa ndodo ya mʼbusa, nyama iliyonse ya 10 izikhala yopatulika kwa Yehova.
-