Numeri 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Yehova analankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai,+ mʼchihema chokumanako.+ Analankhula naye pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri mʼchaka chachiwiri, atatuluka mʼdziko la Iguputo.+ Iye anati:
1 Yehova analankhula ndi Mose mʼchipululu cha Sinai,+ mʼchihema chokumanako.+ Analankhula naye pa tsiku loyamba la mwezi wachiwiri mʼchaka chachiwiri, atatuluka mʼdziko la Iguputo.+ Iye anati: