-
Numeri 1:44Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
44 Awa ndi amuna amene Mose ndi Aroni anawalemba mayina mothandizidwa ndi atsogoleri 12 a Isiraeli. Mtsogoleri aliyense ankaimira nyumba ya makolo ake.
-