Numeri 1:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Aisiraeli azimanga matenti awo mogwirizana ndi msasa wawo, munthu aliyense mogwirizana ndi gulu lake la mafuko atatu,+ potengera magulu awo.*
52 Aisiraeli azimanga matenti awo mogwirizana ndi msasa wawo, munthu aliyense mogwirizana ndi gulu lake la mafuko atatu,+ potengera magulu awo.*