Numeri 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako pazibwera fuko la Zebuloni. Mtsogoleri wa ana a Zebuloni ndi Eliyabu,+ mwana wa Heloni.