Numeri 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mabanja a Agerisoni ankamanga misasa yawo kumbuyo kwa chihema,+ mbali yakumadzulo.