Numeri 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Muwerenge ana onse a Kohati+ mwa ana a Levi, potengera mabanja awo komanso nyumba za makolo awo.