Numeri 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Utumiki umene ana a Kohati azigwira mʼchihema chokumanako,+ womwe ndi utumiki wopatulika koposa, ndi uwu:
4 Utumiki umene ana a Kohati azigwira mʼchihema chokumanako,+ womwe ndi utumiki wopatulika koposa, ndi uwu: