Numeri 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Akatero, aziziphimba ndi nsalu yofiira kwambiri, ndiponso aziphimba tebulolo ndi zikopa za akatumbu. Kenako azibwezeretsa mʼmalo mwake ndodo zake zonyamulira.+
8 Akatero, aziziphimba ndi nsalu yofiira kwambiri, ndiponso aziphimba tebulolo ndi zikopa za akatumbu. Kenako azibwezeretsa mʼmalo mwake ndodo zake zonyamulira.+