Numeri 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, aziphimba guwa lansembe lagolide+ ndi nsalu yabuluu. Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu, nʼkubwezeretsa mʼmalo mwake ndodo zake zonyamulira.+
11 Kenako, aziphimba guwa lansembe lagolide+ ndi nsalu yabuluu. Aziliphimbanso ndi zikopa za akatumbu, nʼkubwezeretsa mʼmalo mwake ndodo zake zonyamulira.+