Numeri 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma uchite izi kuti iwo asaphedwe chifukwa choyandikira zinthu zopatulika koposa:+ Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihemacho, ndipo munthu aliyense azimugawira ntchito ndi katundu woti anyamule.
19 Koma uchite izi kuti iwo asaphedwe chifukwa choyandikira zinthu zopatulika koposa:+ Aroni ndi ana ake azilowa mʼchihemacho, ndipo munthu aliyense azimugawira ntchito ndi katundu woti anyamule.