Numeri 4:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Aroni ndi ana ake aziyangʼanira ntchito imene ana a Gerisoni+ akuchita komanso katundu amene akunyamula. Aziwauza ntchito zimene azigwira ndi katundu amene azinyamula.
27 Aroni ndi ana ake aziyangʼanira ntchito imene ana a Gerisoni+ akuchita komanso katundu amene akunyamula. Aziwauza ntchito zimene azigwira ndi katundu amene azinyamula.