Numeri 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Mose ndi Aroni pamodzi ndi atsogoleri+ a anthuwo, anawerenga ana a Kohati+ potengera mabanja awo ndi nyumba za makolo awo.
34 Kenako Mose ndi Aroni pamodzi ndi atsogoleri+ a anthuwo, anawerenga ana a Kohati+ potengera mabanja awo ndi nyumba za makolo awo.