Numeri 4:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+
45 Amenewa ndi anthu amene anawerengedwa kuchokera mʼmabanja a ana a Merari, amene Mose ndi Aroni anawawerenga pomvera zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.+