-
Numeri 4:49Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
49 Anthuwa anawerengedwa pomvera zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose, aliyense mogwirizana ndi utumiki wake komanso katundu amene ankanyamula. Anawerengedwa mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
-