Numeri 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma ana a Kohati sanawapatse zinthu zimenezi, chifukwa ntchito yawo inali yokhudza utumiki wapamalo oyera.+ Iwo ankanyamula zinthu zopatulika pamapewa awo.+
9 Koma ana a Kohati sanawapatse zinthu zimenezi, chifukwa ntchito yawo inali yokhudza utumiki wapamalo oyera.+ Iwo ankanyamula zinthu zopatulika pamapewa awo.+