Numeri 7:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anaperekanso kapu imodzi* yagolide yolemera masekeli 10, yodzaza ndi zofukiza.