Numeri 7:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Komanso anapereka ngʼombe yaingʼono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo ndi mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+
57 Komanso anapereka ngʼombe yaingʼono yamphongo imodzi, nkhosa imodzi yamphongo ndi mwana wa nkhosa mmodzi wamphongo wosapitirira chaka chimodzi. Nyama zimenezi zinali za nsembe yopsereza.+