-
Numeri 7:86Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
86 Anaperekanso makapu 12 agolide odzaza ndi zofukiza. Kapu iliyonse inali yolemera masekeli 10, mogwirizana ndi muyezo wa sekeli lakumalo oyera. Golide yense wa makapu onsewa anali wolemera masekeli 120.
-