Numeri 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Azikonza nsembeyo mʼmwezi wachiwiri+ pa tsiku la 14, madzulo kuli kachisisira.* Azidya nyama ya nsembeyo pamodzi ndi mikate yopanda zofufumitsa, ndiponso masamba owawa.+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:11 Nsanja ya Olonda,2/1/1993, tsa. 31
11 Azikonza nsembeyo mʼmwezi wachiwiri+ pa tsiku la 14, madzulo kuli kachisisira.* Azidya nyama ya nsembeyo pamodzi ndi mikate yopanda zofufumitsa, ndiponso masamba owawa.+