Numeri 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho, gulu la mafuko atatu la ana a Yuda ndi limene linali loyamba kunyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.
14 Choncho, gulu la mafuko atatu la ana a Yuda ndi limene linali loyamba kunyamuka potengera magulu awo.* Mtsogoleri wa gululi anali Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.