Numeri 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Komabe Mose anamupempha kuti: “Chonde musatisiye, chifukwa inu mukudziwa bwino kumene tingamange msasa mʼchipululu muno, ndipo mungamatilondolere.*
31 Komabe Mose anamupempha kuti: “Chonde musatisiye, chifukwa inu mukudziwa bwino kumene tingamange msasa mʼchipululu muno, ndipo mungamatilondolere.*